Cholinga chinali chiyani?
Zotsatira zake zinali zotani?
Kodi zotsatira zake zinali zosiyana bwanji ndi zomwe mumafuna kuti mukwaniritse poyamba??
Kodi inuyo munaphunzirapo chiyani??
Kodi ena angaphunzire chiyani pa kulephera kwanu?
Kodi mungakambirane zolephera m'dera lanu?